Introductions & The Greatest Musical Showdown in Southern Africa
August 18th 2008 First I'll introduce myself -
Dzina langa ndi Joanna Raeside, ndimachokera ku Scotland. Ndili ndi zaka 29. Ndidabwera ku Malawi mwezi wasanu kugwira ntchito ku PointCare. Ndimakhala ku St Gabriel's Hospital ku Namitete. Ndikufuna kuphunzira kuyankhula, kuwelenga ndi kulemba Chichewa. Pang'ono pang'ono....
(My name is Joanna Raeside. I'm from Scotland. I am 29 years old. I came to Malawi in
... read more